Return to newsletter.

Soccer helps adopted Malawi players adjust to life in America

Joseph Griffin, 13

[In Seattle], my first soccer team was on a recreation team. I had a lot of fun on the team. We wear soccer uniforms here when playing soccer. I had to get use to playing soccer with shoes on. Most of the soccer fields are well taken care of and most of them are grass fields or turf fields. I do not play on a select team. I play forward and I like to score goals.

[In Malawi], soccer is the most popular sport that boys and men like to play. Boys and men can play together for fun as long as they boy is skilled. The girls don't play a lot of football. When the kids or adults play soccer for fun, they don't wear soccer uniforms. Most of the kids don't have enough money to buy an inflated ball, so they make their own balls out of plastic bags and play with them.

Timu yo yambilila imene ndinakhala inali yosavuta. Ndiuali wo sangalala patimuyo. Tima vala ma yunifomu ampila kuno tikama sewela mpila ndi ta vala nsapato. Posewelela mpila pake amasamalapo bwino, ndiponso posewelela pa mbili ndipa kapapinga kapena kapinga wa chi zungi. Panopa ndimasewela patimu yoti umafunika utchuzidwe kuti ukhale pa timuyo. Ndi ma sewela kutsogolo ndiponso ndima konda kuchinya.

Mpila ndi wotchuka kwambili umene anyamata ndi azibambo amakonda ku sewela. Anyamato ndi azibambo atha ku sewela limodzi ngati mwanayo amatha. Atsikana sama sewela mpila kwambili. Momwe anyamata kapena adzibambo akamasewela mpila mongo sewela, samavala yunifomu ya mphila. Ana ambili alibe ndalamazoti agulile mpila wopopa, ndiye amapanga yawo ndi mapepala a plastic ndiku sewela nawo.


Moses Griffin, 16

Seattle soccer is good because we have everything important when playing soccer. When we are playing we put on cleats and shin guards. We also put on our soccer uniforms. Each team has a coach. When I have things like these, they encourage me that in the future I can play professional soccer.

Most kids in Malawi like to play soccer. They have the skill of playing soccer. The football fields that the kids play on are not in good condition. They are dirt fields. Only professional soccer players play on grass or turf. Most of the kids play barefooted because they don't have money to buy boots. I once lost my toenail while playing barefoot. But I did not stop playing soccer because I like it.

Mpila wamiyendo waku Seattle uli bwino, chifukwa tili ndi chinachilichonse chofunika posewela mpila. Tika masewela timavala mabuti ndi mapadi ampila. Komanso timavala yunifomu ya mpila. Tilinso ndi ma kochi. Pamene ndili ndi zonsezi zima ndilimbikitsa kuti mtsogolo ndi zasewela ndimadolo ampila.

Ana ambiri ku Malawi amakonda kusewela mpila wa miyendo. Ali ndi luso losewela mpila. Koma ma galaundi omwe ana amasewelelapo siabwino. Pali dothi lokha lokha. Ma dolo ampila ndi omwe amasewerela pa kapinga. Ana ambiri amasewela opanda ma buti, chifukwa alibe ndalama zoti agule ma buti. Ndina chosapo chikhadaba chakuphazi chifukwa chosewela opanda buti. koma sindinasiye kusewela chifukwa ndimakonda kusewela mpila.


Yohane Griffin, 11

Soccer in Seattle is fun and kind of different. In Seattle I can play on a soccer team. I also can play with my friends. I have a nice coach that is fun to hang around with. I also have to wear shin guards and cleats to play.

Soccer in Malawi is a little different from how they do it here. In Malawi we play bare-foot and we use paper bags to make soccer balls. Only a few kids have boots to use. Kids that really play soccer a lot are the boys. Girls don't play football as much as the boys.

Mpila mu Seattle ndi wobeba ndiponso ndi wosiyana. Mu Seattle nditha ku sewela pa timu. Ndithaso ku sewela ndi anzanga. Ndili ndi akochi abwino ku khala nawo. Ndima funika ndizivala ma shin guards ndi ma buti kuti ndisewele kuno.

Mpila ku Malawi ndi wosiyana pang'ono ndi momwe ama sewelela kuno. Ku Malawi tima sewela opanda nsapato komanso tima uzila ma pepala a plastiki kuti ti pange mipila. Ana ochepa ali ndi ma buti.Ana omwe amakonda ku sewela mpila kwambili ndi anyamata.


Yona Griffin, 18

Soccer in Seattle is well organized and equipped and largely supported, in the sense that are a lot of playgrounds which are turf and in good condition. Here, if you are to go and play for a team, you have to try out. All age groups have their own different teams.

Soccer is well known in Malawi as the sport that brings different tribes together. However, [it is] a developing country that is landlocked and has a population of 14 million people. The youth of Malawi are not supported to play soccer, in such a way that they play without shoes, on bare ground and [with] no soccer balls; if any, they make them out of plastic bags. Last but not least, they have no soccer uniforms. During game time and practice, one side has to take off their shirts for easy recognition.

Mpila ku Seattle ndi wadongosolo, chilichonse choyeneleza chilipo. Komonso ndi wothandizidwa mwaunyinji. Ngati ukufuna kusewela pa timu, amakuyesa kaye. Ndiponso achinyamata amisinkhu yosiyanasiyana oli ndi matimu awo.

Mpila ndi mosewela odziwika bwino ku Malawi,masewilo omwe omabweletsa mitundu ya antnu pamodzi. Malawi ndi dziko lomwe lkutukuka kume,ndipo ili ndi chiwelengelo cha anthu chokwana. 14 million ngakhale izi zili chomwe-chi, anyamata sakuthandizidwa kuti asewele mpila, ena amasewela opanda sapoto, amasela pa mbalanganda komonso mpila omwe amasewela amapanga kuchokela kumapepala (mpila wa chikulinga). Matimu ena alibe majezi,akamasewela amachita kuvula malaya kuti azidziwana.

 
Washington Youth Soccer

Washington Youth Soccer • 500 S. 336th St. Suite 100 • Federal Way, WA 98003
1-877-424-4318 (Toll Free) • (253) 4-SOCCER (476-2237)

PlayOn! is published by Varsity Communications, Inc.
12510 33rd Ave NE, Suite 300 Seattle WA 98125 206-367-2420
For advertising information, please email Brent Vander Mey at Varsity Communications, Inc.

Top | Washington Youth Soccer Homepage